Toyota 4Runner
KasunguMWK 10,000
USD 9
tangazo limeundwaMwezi Wa Saba 11
Inaonekana355
tangazo limeundwaMwezi Wa Saba 11
Inaonekana355
Make an offer
KuhusuToyota 4Runner
InjiniN/A
GearboxManual
MwakaN/A
RangiWhite
Aina ya umboSaloons
Aina ya mafutaDiesel
KiyoyoziNdiyo
Aina ya UsukaniKulia
HaliIlio tumika
Wauzaji maoni
Onyesha zaidi
Safety Notice
- Do not under any circumstances pay in advance.
- Check the car carefully before you buy it. Ask for inspection certificates.
- Check ownership and registration details as well as a vehicle logbook.
- Meet at a safe and public location and bring someone with you.
- Pay after you collect the car. Always request proof of purchase (transfer receipt, email..)
- Look out for significantly undervalued cars. If it looks too good to be true, it probably is.
MWK 10,000
USD 9
DARESALAM CAR COLLECTION SERVICE
Lero tili kuno ku Kasungu Teachers Training College kupereka galimoto iyi Toyota Blade kwa Mr Ophrious Kulira Mwarly amene anatidalira ndikuti khulupilira ndi ntchito imeneyi yokatenga galimoto yi ku Daresalam mdziko la Tanzania nkudzawapatsa kuno kunyumba kwao ku Kasungu TTC. Ulemu wanu bwana Ophrious, zikomo potidalira, Mulungu akudalitseni pamene mukhala mukugwiritsa ntchito mdalitso wanuwu.
NDI IFE NDI ZOTHEKA, KULI KONSE PALI PONSE KUNO KU MALAWI TIMAFIKA.
Ndife ma Driver a galimoto lililonse, timakatenga magalimoto Ku Daresalam ndikubweretsa kuno ku mudzi pa mtengo wabwino
0999544144 / 0888666966
Chisomo pa Chisomo