DARESALAM CAR COLLECTION SERVICE Lero tili kuno ku Kasungu Teachers Training College kupereka galimoto iyi Toyota Blade kwa Mr Ophrious Kulira Mwarly amene anatidalira ndikuti khulupilira ndi ntchito imeneyi yokatenga galimoto yi ku Daresalam mdziko la Tanzania nkudzawapatsa kuno kunyumba kwao ku Kasungu TTC. Ulemu wanu bwana Ophrious, zikomo potidalira, Mulungu akudalitseni pamene mukhala mukugwiritsa ntchito mdalitso wanuwu. NDI IFE NDI ZOTHEKA, KULI KONSE PALI PONSE KUNO KU MALAWI TIMAFIKA. Ndife ma Driver a galimoto lililonse, timakatenga magalimoto Ku Daresalam ndikubweretsa kuno ku mudzi pa mtengo wabwino 0999544144 / 0888666966 Chisomo pa Chisomo